-
1 Mafumu 9:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno Hiramu anachoka ku Turo nʼkupita kukaona mizinda imene Solomo anamupatsa, koma ataiona sinamusangalatse.
-