1 Mafumu 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo anati: “Mʼbale wanga, mizinda imene wandipatsayi ubwino wake uli pati?” Choncho mizindayo anaitchula kuti Dziko la Kabulu* mpaka lero.
13 Ndipo anati: “Mʼbale wanga, mizinda imene wandipatsayi ubwino wake uli pati?” Choncho mizindayo anaitchula kuti Dziko la Kabulu* mpaka lero.