1 Mafumu 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Katatu pachaka,+ Solomo ankapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano paguwa lansembe limene anamangira Yehova.+ Ankaperekanso nsembe zautsi paguwa lansembe lomwe linali pamaso pa Yehova. Choncho anamaliza kumanga nyumbayo.+
25 Katatu pachaka,+ Solomo ankapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano paguwa lansembe limene anamangira Yehova.+ Ankaperekanso nsembe zautsi paguwa lansembe lomwe linali pamaso pa Yehova. Choncho anamaliza kumanga nyumbayo.+