1 Mafumu 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mfumu Solomo inapanganso zombo ku Ezioni-geberi+ pafupi ndi Eloti, pagombe la Nyanja Yofiira, mʼdziko la Edomu.+
26 Mfumu Solomo inapanganso zombo ku Ezioni-geberi+ pafupi ndi Eloti, pagombe la Nyanja Yofiira, mʼdziko la Edomu.+