1 Mafumu 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mfumukaziyo inafika ku Yerusalemu ndi anthu ambiri oiperekeza.+ Inabwera ndi ngamila zitanyamula mafuta a basamu,+ golide wambiri ndi miyala yamtengo wapatali. Inafika kwa Solomo nʼkuyamba kulankhula naye zonse zimene zinali mumtima mwake. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:2 Nsanja ya Olonda,7/1/1999, tsa. 30
2 Mfumukaziyo inafika ku Yerusalemu ndi anthu ambiri oiperekeza.+ Inabwera ndi ngamila zitanyamula mafuta a basamu,+ golide wambiri ndi miyala yamtengo wapatali. Inafika kwa Solomo nʼkuyamba kulankhula naye zonse zimene zinali mumtima mwake.