1 Mafumu 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova anauza Solomo kuti: “Chifukwa chakuti wachita zimenezi ndipo sunasunge pangano langa ndi malamulo amene ndinakupatsa, ndithu ndidzangʼamba ufumuwu kuuchotsa kwa iwe nʼkuupereka kwa mtumiki wako.+
11 Ndiyeno Yehova anauza Solomo kuti: “Chifukwa chakuti wachita zimenezi ndipo sunasunge pangano langa ndi malamulo amene ndinakupatsa, ndithu ndidzangʼamba ufumuwu kuuchotsa kwa iwe nʼkuupereka kwa mtumiki wako.+