1 Mafumu 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe, chifukwa cha bambo ako Davide, sindichita zimenezi iwe uli moyo. Ufumuwu ndidzaungʼamba nʼkuuchotsa mʼmanja mwa mwana wako,+
12 Komabe, chifukwa cha bambo ako Davide, sindichita zimenezi iwe uli moyo. Ufumuwu ndidzaungʼamba nʼkuuchotsa mʼmanja mwa mwana wako,+