-
1 Mafumu 11:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Koma Hadadi ndi Aedomu ena omwe anali atumiki a bambo ake, anathawira ku Iguputo. Pa nthawiyi nʼkuti Hadadi ali kamnyamata.
-