1 Mafumu 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo ananyamuka ku Midiyani nʼkupita ku Parana.+ Kumeneko anatenga anthu ena nʼkukafika ku Iguputo kwa Farao mfumu ya Iguputo. Faraoyo anapatsa Hadadi nyumba ndi malo komanso ankamupatsa chakudya.
18 Iwo ananyamuka ku Midiyani nʼkupita ku Parana.+ Kumeneko anatenga anthu ena nʼkukafika ku Iguputo kwa Farao mfumu ya Iguputo. Faraoyo anapatsa Hadadi nyumba ndi malo komanso ankamupatsa chakudya.