-
1 Mafumu 11:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Farao ankamukonda kwambiri Hadadi moti mpaka anamʼpatsa mkazi. Mkaziyo anali mngʼono wake wa Tapenesi, mkazi wa Farao.
-