1 Mafumu 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Patapita nthawi, mngʼono wake wa Tapenesi anaberekera Hadadi mwana wamwamuna dzina lake Genubati. Tapenesi anamutenga* nʼkumamulera mʼnyumba ya Farao ndipo Genubati ankakhala mʼnyumba ya Farao pamodzi ndi ana a Farao.
20 Patapita nthawi, mngʼono wake wa Tapenesi anaberekera Hadadi mwana wamwamuna dzina lake Genubati. Tapenesi anamutenga* nʼkumamulera mʼnyumba ya Farao ndipo Genubati ankakhala mʼnyumba ya Farao pamodzi ndi ana a Farao.