1 Mafumu 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Hadadi ali ku Iguputo, anamva kuti Davide, mofanana ndi makolo ake, anamwalira+ ndiponso kuti Yowabu mkulu wa asilikali anamwaliranso.+ Choncho Hadadi anapempha Farao kuti: “Kodi mungandilole kuti ndizipita kwathu?”
21 Hadadi ali ku Iguputo, anamva kuti Davide, mofanana ndi makolo ake, anamwalira+ ndiponso kuti Yowabu mkulu wa asilikali anamwaliranso.+ Choncho Hadadi anapempha Farao kuti: “Kodi mungandilole kuti ndizipita kwathu?”