-
1 Mafumu 11:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Rezoni ankalimbana ndi Aisiraeli masiku onse a Solomo, ndipo ankawachitira zoipa kuwonjezera pa zoipa zimene Hadadi ankawachitira. Rezoni ankadana kwambiri ndi Aisiraeli pa nthawi imene iye ankalamulira ku Siriya.
-