1 Mafumu 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma sindidzachotsa ufumu wonse mʼmanja mwake. Ndidzamulola kukhalabe mtsogoleri masiku onse a moyo wake chifukwa cha Davide mtumiki wanga amene ndinamusankha,+ popeza Davide anasunga malamulo anga.
34 Koma sindidzachotsa ufumu wonse mʼmanja mwake. Ndidzamulola kukhalabe mtsogoleri masiku onse a moyo wake chifukwa cha Davide mtumiki wanga amene ndinamusankha,+ popeza Davide anasunga malamulo anga.