1 Mafumu 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Rehobowamu atamva zimenezi anauza anthuwo kuti: “Pitani kaye ndipo mukabwerenso pakatha masiku atatu.” Choncho anthuwo anapitadi.+
5 Rehobowamu atamva zimenezi anauza anthuwo kuti: “Pitani kaye ndipo mukabwerenso pakatha masiku atatu.” Choncho anthuwo anapitadi.+