-
1 Mafumu 12:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iwo anamuuza kuti: “Ngati lero mungakhale mtumiki wa anthuwa, kumvera zimene apempha ndiponso kuwayankha bwino, iwo adzakhala atumiki anu nthawi zonse.”
-