1 Mafumu 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa tsiku lachitatu, Yerobowamu ndi anthu onse anapita kwa Rehobowamu, mogwirizana ndi zimene mfumuyo inanena kuti: “Mukabwerenso pakatha masiku atatu.”+
12 Pa tsiku lachitatu, Yerobowamu ndi anthu onse anapita kwa Rehobowamu, mogwirizana ndi zimene mfumuyo inanena kuti: “Mukabwerenso pakatha masiku atatu.”+