1 Mafumu 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mfumuyo inayankha anthuwo mwaukali ndipo sinamvere malangizo a anthu achikulire* aja.