1 Mafumu 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako munthu wa Mulunguyo anapereka chizindikiro. Iye anati: “Chizindikiro chimene Yehova wapereka ndi ichi: Guwa lansembeli lingʼambika pakati ndipo phulusa* limene lili paguwali litayika.”
3 Kenako munthu wa Mulunguyo anapereka chizindikiro. Iye anati: “Chizindikiro chimene Yehova wapereka ndi ichi: Guwa lansembeli lingʼambika pakati ndipo phulusa* limene lili paguwali litayika.”