-
1 Mafumu 13:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako guwa lansembelo linangʼambika ndipo phulusa linatayika mogwirizana ndi chizindikiro chimene munthu wa Mulungu woonayo anapereka, malinga ndi mawu a Yehova.
-