-
1 Mafumu 13:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndiyeno panali mneneri wina wokalamba yemwe ankakhala ku Beteli. Ana ake anabwera nʼkumufotokozera zonse zimene munthu wa Mulungu woona uja anachita ku Beteli komanso zomwe anauza mfumu. Atamufotokozera zimenezi,
-