-
1 Mafumu 13:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 bamboyo anafunsa anawo kuti: “Munthuyo wadzera njira iti?” Anawo analozera bamboyo njira imene munthu wa Mulungu woona wochokera ku Yuda uja anadzera.
-