-
1 Mafumu 13:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako bamboyo anauza anawo kuti: “Ndimangireni chishalo pabulu.” Anawo anamangiradi bambo awowo chishalo ndipo iwo anakwera buluyo.
-