1 Mafumu 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero, anatsatira munthu wa Mulungu woona uja ndipo anamʼpeza atakhala pansi pa mtengo waukulu. Ndiyeno anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe munthu wa Mulungu woona amene wachokera ku Yuda?”+ Munthuyo anayankha kuti: “Inde, ndi ineyo.”
14 Atatero, anatsatira munthu wa Mulungu woona uja ndipo anamʼpeza atakhala pansi pa mtengo waukulu. Ndiyeno anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe munthu wa Mulungu woona amene wachokera ku Yuda?”+ Munthuyo anayankha kuti: “Inde, ndi ineyo.”