1 Mafumu 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 koma wabwerera kuti udye chakudya ndi kumwa madzi kumalo amene iye anakuuza kuti: “Usakadye chakudya kapena kumwa madzi,” mtembo wako sudzaikidwa mʼmanda a makolo ako.’”+
22 koma wabwerera kuti udye chakudya ndi kumwa madzi kumalo amene iye anakuuza kuti: “Usakadye chakudya kapena kumwa madzi,” mtembo wako sudzaikidwa mʼmanda a makolo ako.’”+