1 Mafumu 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako mneneri wa ku Yudayo ananyamuka nʼkumapita. Koma mkango unamupeza panjira nʼkumupha,+ ndipo mtembo wake unali pamsewu. Bulu ndi mkangowo zinaima pambali pa mtembowo.
24 Kenako mneneri wa ku Yudayo ananyamuka nʼkumapita. Koma mkango unamupeza panjira nʼkumupha,+ ndipo mtembo wake unali pamsewu. Bulu ndi mkangowo zinaima pambali pa mtembowo.