-
1 Mafumu 13:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Anthu ena amene ankadutsa, anaona mtembowo uli pamsewupo, mkango utaima pambali pake. Anthuwo atafika mumzinda womwe mneneri wokalamba uja ankakhala, anafotokoza zomwe anaonazo.
-