26 Mneneri amene anakabweza munthu uja atamva nkhaniyi, nthawi yomweyo anati: “Ndi munthu wa Mulungu woona amene sanamvere lamulo la Yehova uja.+ Choncho Yehova wamupereka kwa mkango kuti umugwire nʼkumupha, mogwirizana ndi mawu amene Yehova anamuuza.”+