-
1 Mafumu 13:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Mneneri wokalambayo ananyamuka nʼkukapeza mtembo wa munthu uja uli pamsewu, bulu ndi mkango zitaima pambali pake. Mkangowo sunadye mtembowo kapena kupha buluyo.
-