1 Mafumu 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkazi wa Yerobowamu anachitadi zimenezo. Ananyamuka kupita ku Silo+ nʼkukafika kunyumba kwa Ahiya. Ahiyayo sankatha kuona chifukwa maso ake anali atachita khungu ndi ukalamba.
4 Mkazi wa Yerobowamu anachitadi zimenezo. Ananyamuka kupita ku Silo+ nʼkukafika kunyumba kwa Ahiya. Ahiyayo sankatha kuona chifukwa maso ake anali atachita khungu ndi ukalamba.