-
1 Mafumu 14:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ahiya atangomva phokoso la mapazi a mkazi wa Yerobowamu pamene ankafika pakhomo anati: “Lowa mkazi wa Yerobowamu. Nʼchifukwa chiyani ukudzisintha kuti usadziwike? Ine ndatumidwa kuti ndikuuze uthenga wopweteka.
-