1 Mafumu 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pita ukauze Yerobowamu kuti, ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ine ndinakukweza pakati pa anthu a mtundu wako kuti ukhale mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli.+
7 Pita ukauze Yerobowamu kuti, ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ine ndinakukweza pakati pa anthu a mtundu wako kuti ukhale mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli.+