-
1 Mafumu 14:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Choncho anamuika mʼmanda ndipo Aisiraeli onse anamulira, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena kudzera mwa mtumiki wake, mneneri Ahiya.
-