1 Mafumu 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nkhani zina zokhudza Abiyamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda.+ Pakati pa Abiyamu ndi Yerobowamu, panachitikanso nkhondo.+
7 Nkhani zina zokhudza Abiyamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda.+ Pakati pa Abiyamu ndi Yerobowamu, panachitikanso nkhondo.+