1 Mafumu 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Abiyamu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide. Ndiyeno mwana wake Asa+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.+
8 Kenako Abiyamu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide. Ndiyeno mwana wake Asa+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.+