1 Mafumu 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anachotsa ngakhalenso agogo ake aakazi a Maaka+ pa udindo wawo wokhala mayi wa mfumu, chifukwa anapanga fano lonyansa kwambiri lolambirira mzati wopatulika.* Asa anagwetsa fanolo+ nʼkukalitentha mʼchigwa cha Kidironi.+
13 Anachotsa ngakhalenso agogo ake aakazi a Maaka+ pa udindo wawo wokhala mayi wa mfumu, chifukwa anapanga fano lonyansa kwambiri lolambirira mzati wopatulika.* Asa anagwetsa fanolo+ nʼkukalitentha mʼchigwa cha Kidironi.+