-
1 Mafumu 15:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 “Pali pangano pakati pa ine ndi iwe ndiponso pakati pa bambo anga ndi bambo ako. Ndakutumizira mphatso ya siliva ndi golide. Bwera udzaphwanye pangano lako ndi Basa mfumu ya Isiraeli kuti achoke mʼdera langa.”
-