1 Mafumu 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye ankachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anatsatira njira ya bambo ake+ komanso machimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha bambo akewo.+
26 Iye ankachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anatsatira njira ya bambo ake+ komanso machimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha bambo akewo.+