-
1 Mafumu 16:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako mtumiki wake Zimiri, amene ankayangʼanira hafu ya asilikali oyenda pa magaleta, anamukonzera chiwembu pamene Ela ankamwa mowa mpaka kuledzera kunyumba ya Ariza ku Tiriza. Ariza anali woyangʼanira banja la mfumu ku Tirizako.
-