-
1 Mafumu 16:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Pa nthawi imeneyi mʼpamene anthu a ku Isiraeli anagawikana mʼmagulu awiri. Gulu lina linkatsatira Tibini mwana wa Ginati ndipo linkafuna kumuveka ufumu ndipo gulu linalo linkatsatira Omuri.
-