-
1 Mafumu 20:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mfumu ya Isiraeli itamva mawu amenewa, inaitanitsa akulu onse amʼdzikolo nʼkuwauza kuti: “Munthuyu watsimikiza mtima kuti atibweretsere tsoka. Ananditumizira uthenga woti akufuna akazi anga, ana anga aamuna, siliva wanga ndi golide wanga, ndipo ine sindinamukanize.”
-