-
1 Mafumu 20:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Beni-hadadi anamva mawu amenewa pamene iye ndi mafumu amene anali naye ankamwa mowa mʼmatenti. Nthawi yomweyo, anauza antchito ake kuti: “Konzekerani nkhondo!” Choncho iwo anakonzekera kukamenyana ndi anthu amumzindawo.
-