1 Mafumu 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mneneri wina anapita kwa Ahabu+ mfumu ya Isiraeli nʼkumuuza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kodi waona chigulu chonsechi? Anthu onsewa ndiwapereka mʼmanja mwako lero ndipo udziwadi kuti ine ndine Yehova.’”+
13 Koma mneneri wina anapita kwa Ahabu+ mfumu ya Isiraeli nʼkumuuza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kodi waona chigulu chonsechi? Anthu onsewa ndiwapereka mʼmanja mwako lero ndipo udziwadi kuti ine ndine Yehova.’”+