-
1 Mafumu 20:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ahabu anafunsa kuti: “Adzagwiritsa ntchito ndani?” Mneneriyo anayankha kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzagwiritsa ntchito atumiki a akalonga oyangʼanira zigawo.’” Kenako Ahabu anafunsa kuti: “Ndani akayambitse nkhondoyo?” Mneneriyo anayankha kuti: “Inuyo.”
-