-
1 Mafumu 20:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ahabu anawerenga atumiki a akalonga oyangʼanira zigawo ndipo anakwana 232. Atamaliza, anawerenganso asilikali onse a Isiraeli ndipo analipo 7,000.
-