-
1 Mafumu 20:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Atumiki a akalonga oyangʼanira zigawo ndi amene anatsogola. Atangofika, Beni-hadadi anatumizako anthu ndipo anthuwo atabwerera anamuuza kuti: “Kwabwera anthu ochokera ku Samariya.”
-