1 Mafumu 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako mneneri uja+ anapita kwa mfumu ya Isiraeli nʼkunena kuti: “Pitani, kalimbitseni asilikali anu ankhondo ndi kuganizira zomwe mudzachite,+ chifukwa kumayambiriro kwa chaka chamawa mfumu ya Siriya idzabweranso kudzamenyana nanu.”+
22 Kenako mneneri uja+ anapita kwa mfumu ya Isiraeli nʼkunena kuti: “Pitani, kalimbitseni asilikali anu ankhondo ndi kuganizira zomwe mudzachite,+ chifukwa kumayambiriro kwa chaka chamawa mfumu ya Siriya idzabweranso kudzamenyana nanu.”+