-
1 Mafumu 20:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Atumiki a mfumu ya Siriya anauza mfumuyo kuti: “Mulungu wawo ndi Mulungu wa mapiri, nʼchifukwa chake anatigonjetsa. Koma ngati titamenyana nawo pamalo afulati tikhoza kuwagonjetsa.
-