1 Mafumu 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Komanso muchite izi: Muchotse mafumu onse+ pa maudindo awo ndipo muike abwanamkubwa mʼmalo mwawo.