-
1 Mafumu 20:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Kenako musonkhanitse asilikali ndipo chiwerengero chawo chikhale chofanana ndi cha asilikali amene anafa aja. Chiwerengero cha mahatchi ndi magaleta chikhalenso chofanana ndi choyamba chija. Tikatero tikamenyane nawo pamalo afulati ndipo ndithu tikawagonjetsa.” Choncho mfumuyo inamvera malangizo awo ndipo inachitadi zimenezo.
-